Numeri 33:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Mukapitikitse anthu onse a m’dzikolo, ndipo mukawononge zifaniziro zawo zonse zamiyala,+ ndi mafano awo onse achitsulo.+ Mukawonongenso malo awo onse opatulika olambirira.+ Deuteronomo 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Koma inu mudzawachitire zotsatirazi: Mudzagwetse maguwa awo ansembe+ ndi kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ Mudzadule+ mizati yawo yopatulika+ ndi kutentha zifaniziro zawo zogoba.+ Deuteronomo 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mudzatenthe zifaniziro zogoba za milungu yawo.+ Usadzalakelake siliva ndi golide wawo+ kapena kudzitengera zinthu zimenezi,+ kuopera kuti zingakutchere msampha,+ chifukwa zimenezi ndi zonyansa+ kwa Yehova Mulungu wako.
52 Mukapitikitse anthu onse a m’dzikolo, ndipo mukawononge zifaniziro zawo zonse zamiyala,+ ndi mafano awo onse achitsulo.+ Mukawonongenso malo awo onse opatulika olambirira.+
5 “Koma inu mudzawachitire zotsatirazi: Mudzagwetse maguwa awo ansembe+ ndi kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ Mudzadule+ mizati yawo yopatulika+ ndi kutentha zifaniziro zawo zogoba.+
25 Mudzatenthe zifaniziro zogoba za milungu yawo.+ Usadzalakelake siliva ndi golide wawo+ kapena kudzitengera zinthu zimenezi,+ kuopera kuti zingakutchere msampha,+ chifukwa zimenezi ndi zonyansa+ kwa Yehova Mulungu wako.