Ekisodo 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inuyo mudzakhala ufumu wanga wa ansembe ndi mtundu wanga woyera.’+ Ukanene mawu amenewa kwa ana a Isiraeli.” Deuteronomo 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti ndinu anthu oyera+ kwa Yehova Mulungu wanu, ndipo Yehova wakusankhani kuti mukhale anthu ake, chuma chake chapadera,+ mwa anthu onse okhala padziko lapansi. Yeremiya 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Isiraeli anali wopatulika kwa Yehova,+ ndipo anali zipatso zoyambirira kwa Iye.”’+ ‘Anthu onse ofuna kumumeza anali kukhala ndi mlandu+ ndipo tsoka linali kuwagwera,’ watero Yehova.”+
6 Inuyo mudzakhala ufumu wanga wa ansembe ndi mtundu wanga woyera.’+ Ukanene mawu amenewa kwa ana a Isiraeli.”
2 Pakuti ndinu anthu oyera+ kwa Yehova Mulungu wanu, ndipo Yehova wakusankhani kuti mukhale anthu ake, chuma chake chapadera,+ mwa anthu onse okhala padziko lapansi.
3 Isiraeli anali wopatulika kwa Yehova,+ ndipo anali zipatso zoyambirira kwa Iye.”’+ ‘Anthu onse ofuna kumumeza anali kukhala ndi mlandu+ ndipo tsoka linali kuwagwera,’ watero Yehova.”+