Deuteronomo 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti iye ndi amene Yehova Mulungu wako wam’sankha pakati pa mafuko anu onse, kuti iye pamodzi ndi ana ake aimirire ndi kutumikira m’dzina la Yehova nthawi zonse.+ 2 Mbiri 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno inu ana anga musapumule,+ chifukwa inu ndi amene Yehova wakusankhani kuti muziima pamaso pake ndi kum’tumikira+ ndiponso kuti mukhalebe atumiki ake+ ndi ofukiza nsembe yautsi.”+
5 Pakuti iye ndi amene Yehova Mulungu wako wam’sankha pakati pa mafuko anu onse, kuti iye pamodzi ndi ana ake aimirire ndi kutumikira m’dzina la Yehova nthawi zonse.+
11 Ndiyeno inu ana anga musapumule,+ chifukwa inu ndi amene Yehova wakusankhani kuti muziima pamaso pake ndi kum’tumikira+ ndiponso kuti mukhalebe atumiki ake+ ndi ofukiza nsembe yautsi.”+