Yona 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndani angadziwe? Mwina Mulungu woona satigwetsera tsoka ndipo asintha maganizo+ ndi kubweza mkwiyo wake woyaka moto, moti satiwononga.”+ Aroma 3:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kapena kodi iye ndi Mulungu wa Ayuda okha?+ Kodi salinso Mulungu wa anthu a mitundu ina?+ Inde, iye alinso Mulungu wa anthu a mitundu ina,+ Aheberi 11:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Mwa chikhulupiriro, Rahabi+ hule lija, sanawonongedwe limodzi ndi anthu amene anachita zinthu mosamvera, chifukwa iye analandira azondi mwamtendere.+
9 Ndani angadziwe? Mwina Mulungu woona satigwetsera tsoka ndipo asintha maganizo+ ndi kubweza mkwiyo wake woyaka moto, moti satiwononga.”+
29 Kapena kodi iye ndi Mulungu wa Ayuda okha?+ Kodi salinso Mulungu wa anthu a mitundu ina?+ Inde, iye alinso Mulungu wa anthu a mitundu ina,+
31 Mwa chikhulupiriro, Rahabi+ hule lija, sanawonongedwe limodzi ndi anthu amene anachita zinthu mosamvera, chifukwa iye analandira azondi mwamtendere.+