Genesis 49:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Koma iwe Yuda,+ abale ako adzakutamanda.+ Dzanja lako lidzakhala pambuyo pa khosi la adani ako.+ Ana a bambo ako adzakugwadira.+ Numeri 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho, a m’chigawo cha mafuko atatu cha ana a Yuda ndiwo anayamba kunyamuka m’magulu awo.+ Mtsogoleri wa asilikali awo anali Naasoni,+ mwana wa Aminadabu. Oweruza 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo Yehova anayankha kuti: “Fuko la Yuda ndilo lidzayamba kupita.+ Ndipo ndidzaperekadi dzikolo m’manja mwawo.” 1 Mbiri 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chifukwa chakuti Yuda+ anali wamphamvu pakati pa abale ake, mwa iye munachokera mtsogoleri,+ koma udindo wa woyamba kubadwa unali wa Yosefe.+
8 “Koma iwe Yuda,+ abale ako adzakutamanda.+ Dzanja lako lidzakhala pambuyo pa khosi la adani ako.+ Ana a bambo ako adzakugwadira.+
14 Choncho, a m’chigawo cha mafuko atatu cha ana a Yuda ndiwo anayamba kunyamuka m’magulu awo.+ Mtsogoleri wa asilikali awo anali Naasoni,+ mwana wa Aminadabu.
2 Pamenepo Yehova anayankha kuti: “Fuko la Yuda ndilo lidzayamba kupita.+ Ndipo ndidzaperekadi dzikolo m’manja mwawo.”
2 Chifukwa chakuti Yuda+ anali wamphamvu pakati pa abale ake, mwa iye munachokera mtsogoleri,+ koma udindo wa woyamba kubadwa unali wa Yosefe.+