Deuteronomo 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Tamverani, Aisiraeli inu: Yehova Mulungu wathu ndi Yehova mmodzi.*+ Salimo 81:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ine Yehova, ndine Mulungu wanu,+Amene ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo.+Tsegulani pakamwa panu ndipo ndidzaikamo chakudya.+ Hoseya 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Koma ine ndine Yehova Mulungu wako kuchokera pamene unali ku Iguputo.+ Panalibe Mulungu wina amene unali kumudziwa kupatulapo ine. Panalibenso mpulumutsi wina kupatulapo ine.+
10 Ine Yehova, ndine Mulungu wanu,+Amene ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo.+Tsegulani pakamwa panu ndipo ndidzaikamo chakudya.+
4 “Koma ine ndine Yehova Mulungu wako kuchokera pamene unali ku Iguputo.+ Panalibe Mulungu wina amene unali kumudziwa kupatulapo ine. Panalibenso mpulumutsi wina kupatulapo ine.+