Deuteronomo 32:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anapitiriza kumuyendetsa pamapiri a dziko lapansi,+Moti anadya zokolola za m’minda.+Anapitirizanso kumudyetsa uchi wochokera m’thanthwe,+Ndi mafuta ochokera m’mwala wa nsangalabwi.+ Salimo 37:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndinali mwana, ndipo tsopano ndakula,+Koma sindinaonepo munthu aliyense wolungama atasiyidwa,+Kapena ana ake akupemphapempha chakudya.+ Chivumbulutso 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anandiuzanso kuti: “Zakwaniritsidwa! Ine ndine Alefa ndi Omega, chiyambi ndi mapeto.+ Aliyense womva ludzu, ndidzamupatsa madzi a m’kasupe wa moyo kwaulere.+
13 Anapitiriza kumuyendetsa pamapiri a dziko lapansi,+Moti anadya zokolola za m’minda.+Anapitirizanso kumudyetsa uchi wochokera m’thanthwe,+Ndi mafuta ochokera m’mwala wa nsangalabwi.+ Salimo 37:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndinali mwana, ndipo tsopano ndakula,+Koma sindinaonepo munthu aliyense wolungama atasiyidwa,+Kapena ana ake akupemphapempha chakudya.+ Chivumbulutso 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anandiuzanso kuti: “Zakwaniritsidwa! Ine ndine Alefa ndi Omega, chiyambi ndi mapeto.+ Aliyense womva ludzu, ndidzamupatsa madzi a m’kasupe wa moyo kwaulere.+
25 Ndinali mwana, ndipo tsopano ndakula,+Koma sindinaonepo munthu aliyense wolungama atasiyidwa,+Kapena ana ake akupemphapempha chakudya.+
6 Anandiuzanso kuti: “Zakwaniritsidwa! Ine ndine Alefa ndi Omega, chiyambi ndi mapeto.+ Aliyense womva ludzu, ndidzamupatsa madzi a m’kasupe wa moyo kwaulere.+