Oweruza 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tsopano Gidiyoni anazindikira kuti anali mngelo wa Yehova.+ Nthawi yomweyo Gidiyoni anati: “Kalanga ine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa! Ndaonana ndi mngelo wa Yehova maso ndi maso.”+
22 Tsopano Gidiyoni anazindikira kuti anali mngelo wa Yehova.+ Nthawi yomweyo Gidiyoni anati: “Kalanga ine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa! Ndaonana ndi mngelo wa Yehova maso ndi maso.”+