Oweruza 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako anayatsa miyuniyo ndi moto, n’kutumiza nkhandwezo m’minda ya Afilisti ya mbewu zosakolola. Choncho anayatsa chilichonse, kuyambira mitolo ya mbewu, mbewu zosakolola, minda ya mpesa mpaka minda ya maolivi.+
5 Kenako anayatsa miyuniyo ndi moto, n’kutumiza nkhandwezo m’minda ya Afilisti ya mbewu zosakolola. Choncho anayatsa chilichonse, kuyambira mitolo ya mbewu, mbewu zosakolola, minda ya mpesa mpaka minda ya maolivi.+