Yoswa 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kum’mwera kwatsala dziko lonse la Akanani. Patsalanso mzinda wa Asidoni+ wotchedwa Meara, mpaka kukafika ku Afeki kumalire a Aamori, Yoswa 19:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Anapitirira mpaka ku Eburoni, Rehobu, Hamoni, Kana, mpaka kumzinda wa anthu ambiri wa Sidoni.+ Oweruza 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mitunduyo ndi olamulira asanu ogwirizana+ a Afilisiti,+ Akanani onse,+ ngakhalenso Asidoni+ ndi Ahivi+ okhala m’phiri la Lebanoni,+ kuchokera kuphiri la Baala-herimoni+ mpaka kumalire a dera la Hamati.+ Oweruza 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Asidoni,+ Aamaleki+ ndi Amidiyani+ atakuponderezani,+ sindinakupulumutseni m’manja mwawo mutafuulira kwa ine?
4 Kum’mwera kwatsala dziko lonse la Akanani. Patsalanso mzinda wa Asidoni+ wotchedwa Meara, mpaka kukafika ku Afeki kumalire a Aamori,
3 Mitunduyo ndi olamulira asanu ogwirizana+ a Afilisiti,+ Akanani onse,+ ngakhalenso Asidoni+ ndi Ahivi+ okhala m’phiri la Lebanoni,+ kuchokera kuphiri la Baala-herimoni+ mpaka kumalire a dera la Hamati.+
12 Asidoni,+ Aamaleki+ ndi Amidiyani+ atakuponderezani,+ sindinakupulumutseni m’manja mwawo mutafuulira kwa ine?