-
Yoswa 9:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Mafumu+ a kutsidya kwa Yorodano anamva zimene zinachitika. Amenewa anali mafumu a Ahiti,+ Aamori, Akanani,+ Aperezi,+ Ahivi ndi Ayebusi.+ Iwo anali kukhala kudera lamapiri, ndiponso ku Sefela, ndi m’mbali monse mwa Nyanja Yaikulu,+ komanso pafupi ndi Lebanoni.+ Mafumu onsewo atangomva zimene zinachitikazo,
-