1 Samueli 14:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Chotero Sauli anayamba kufunsira kwa Mulungu, kuti: “Kodi ndipite kwa Afilisiti?+ Kodi muwapereka m’manja mwa Isiraeli?”+ Koma Mulungu sanamuyankhe pa tsikuli.+ Salimo 28:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Adalitsike Yehova, chifukwa wamva kuchonderera kwanga.+
37 Chotero Sauli anayamba kufunsira kwa Mulungu, kuti: “Kodi ndipite kwa Afilisiti?+ Kodi muwapereka m’manja mwa Isiraeli?”+ Koma Mulungu sanamuyankhe pa tsikuli.+