Yoswa 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano Yoswa anali atakalamba, ndipo anali ndi zaka zambiri.+ Choncho Yehova anamuuza kuti: “Iweyo wakalamba ndipo uli ndi zaka zambiri, koma dziko loti lilandidwe likadali lalikulu.+ Yoswa 23:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Munthu mmodzi yekha wa inu adzathamangitsa anthu 1,000,+ chifukwa Yehova Mulungu wanu ndiye akukumenyerani nkhondo,+ monga mmene anakulonjezerani.+
13 Tsopano Yoswa anali atakalamba, ndipo anali ndi zaka zambiri.+ Choncho Yehova anamuuza kuti: “Iweyo wakalamba ndipo uli ndi zaka zambiri, koma dziko loti lilandidwe likadali lalikulu.+
10 Munthu mmodzi yekha wa inu adzathamangitsa anthu 1,000,+ chifukwa Yehova Mulungu wanu ndiye akukumenyerani nkhondo,+ monga mmene anakulonjezerani.+