1 Samueli 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano ufumu wako sukhalitsa.+ Yehova apeza munthu wapamtima pake,+ ndipo Yehova amuika kukhala mtsogoleri+ wa anthu ake chifukwa iwe sunasunge zimene Yehova anakulamula.”+ 1 Samueli 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye anatumadi munthu kukam’tenga. Mnyamatayo anali wamaonekedwe ofiirira,+ mnyamata wa maso okongola, ndiponso wooneka bwino. Pamenepo Yehova anati: “Ndi ameneyu! Nyamuka umudzoze.”+ 1 Samueli 28:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yehova achitadi zimene ananena kudzera mwa ine, ndipo Yehova ang’amba ufumuwu kuuchotsa kwa iwe+ ndi kuupereka kwa mnzako Davide.+ Machitidwe 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Atamuchotsa ameneyu,+ anawapatsa Davide monga mfumu yawo.+ Iyeyu Mulungu anamuchitira umboni kuti, ‘Ndapeza Davide mwana wa Jese,+ munthu wapamtima panga.+ Ameneyu adzachita zonse zimene ine ndikufuna.’+
14 Tsopano ufumu wako sukhalitsa.+ Yehova apeza munthu wapamtima pake,+ ndipo Yehova amuika kukhala mtsogoleri+ wa anthu ake chifukwa iwe sunasunge zimene Yehova anakulamula.”+
12 Iye anatumadi munthu kukam’tenga. Mnyamatayo anali wamaonekedwe ofiirira,+ mnyamata wa maso okongola, ndiponso wooneka bwino. Pamenepo Yehova anati: “Ndi ameneyu! Nyamuka umudzoze.”+
17 Yehova achitadi zimene ananena kudzera mwa ine, ndipo Yehova ang’amba ufumuwu kuuchotsa kwa iwe+ ndi kuupereka kwa mnzako Davide.+
22 Atamuchotsa ameneyu,+ anawapatsa Davide monga mfumu yawo.+ Iyeyu Mulungu anamuchitira umboni kuti, ‘Ndapeza Davide mwana wa Jese,+ munthu wapamtima panga.+ Ameneyu adzachita zonse zimene ine ndikufuna.’+