Salimo 120:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 120 Ndinafuulira Yehova m’masautso anga,+Ndipo iye anandiyankha.+ Salimo 142:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 142 Ndinafuulira Yehova kuti andithandize.+Ndinafuulira Yehova kuti andikomere mtima.+ Yona 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 kuti:“Pamene ndinali m’masautso ndinaitana Yehova,+ ndipo anandiyankha.+Ndinafuula kupempha thandizo ndili m’Manda* akuya.+Ndipo inu munamva mawu anga.+
2 kuti:“Pamene ndinali m’masautso ndinaitana Yehova,+ ndipo anandiyankha.+Ndinafuula kupempha thandizo ndili m’Manda* akuya.+Ndipo inu munamva mawu anga.+