Salimo 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Dziko lapansi linayamba kugwedezekera uku ndi uku ndiponso kutekeseka.+Maziko a mapiri anagwedezeka,+Anagwedezekera uku ndi uku chifukwa Mulungu anakwiya.+ Salimo 77:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Phokoso la bingu lanu linali ngati la mawilo a galeta.+Mphezi zinaunika padziko.+Ndipo dziko lapansi linagwedezeka ndi kuyamba kunjenjemera.+ Salimo 97:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mphezi zake zinawalitsa dziko lapansi.+Dziko linaona ndipo linachita mantha kwambiri.+
7 Dziko lapansi linayamba kugwedezekera uku ndi uku ndiponso kutekeseka.+Maziko a mapiri anagwedezeka,+Anagwedezekera uku ndi uku chifukwa Mulungu anakwiya.+
18 Phokoso la bingu lanu linali ngati la mawilo a galeta.+Mphezi zinaunika padziko.+Ndipo dziko lapansi linagwedezeka ndi kuyamba kunjenjemera.+