1 Samueli 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho Samueli anatenga nyanga ya mafuta+ ndi kum’dzoza pakati pa abale ake. Zitatero, mzimu wa Yehova unayamba kugwira ntchito pa Davide kuyambira tsiku limenelo mpaka m’tsogolo.+ Kenako Samueli ananyamuka kupita ku Rama.+ Salimo 89:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndapeza Davide mtumiki wanga,+Ndipo ndamudzoza ndi mafuta anga opatulika.+
13 Choncho Samueli anatenga nyanga ya mafuta+ ndi kum’dzoza pakati pa abale ake. Zitatero, mzimu wa Yehova unayamba kugwira ntchito pa Davide kuyambira tsiku limenelo mpaka m’tsogolo.+ Kenako Samueli ananyamuka kupita ku Rama.+