27 Nyengo yolira maliro+ itatha, nthawi yomweyo Davide anatumiza nthumwi kukatenga Bati-seba ndi kubwera naye kunyumba kwake, ndipo anakhala mkazi wake.+ Patapita nthawi, anamuberekera mwana wamwamuna. Koma zimene Davide anachitazi zinamuipira kwambiri Yehova.+