2 Samueli 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako Simeyi+ mwana wa Gera,+ wa fuko la Benjamini, wochokera ku Bahurimu,+ pamodzi ndi amuna a ku Yuda anapita mofulumira kukakumana ndi Mfumu Davide. 1 Mafumu 2:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Ndiyeno mfumuyo inapitiriza kuuza Simeyi kuti: “Iweyo wekha ukudziwa bwino mumtima mwako zoipa zonse zimene unachitira Davide bambo anga.+ Yehova akubwezera ndithu pamutu pako zoipa zimene unachita.+
16 Kenako Simeyi+ mwana wa Gera,+ wa fuko la Benjamini, wochokera ku Bahurimu,+ pamodzi ndi amuna a ku Yuda anapita mofulumira kukakumana ndi Mfumu Davide.
44 Ndiyeno mfumuyo inapitiriza kuuza Simeyi kuti: “Iweyo wekha ukudziwa bwino mumtima mwako zoipa zonse zimene unachitira Davide bambo anga.+ Yehova akubwezera ndithu pamutu pako zoipa zimene unachita.+