2 Samueli 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno Mfumu Davide inafika ku Bahurimu.+ Kumeneko inaona mwamuna wina wa m’banja la Sauli, dzina lake Simeyi,+ mwana wa Gera akutuluka ndipo anali kulankhula mawu onyoza.+ 2 Samueli 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo Davide ndi amuna amene anali kuyenda naye anapitiriza kuyenda mumsewu. Simeyi anali kuyenda m’mbali mwa phiri pafupi ndi Davide ndipo anali kuyenda akulankhula mawu onyoza.+ Iye analinso kuponya miyala akuyenda m’mbali mwa phirimo pafupi ndi Davide ndiponso anali kuwaza fumbi lambiri.+
5 Ndiyeno Mfumu Davide inafika ku Bahurimu.+ Kumeneko inaona mwamuna wina wa m’banja la Sauli, dzina lake Simeyi,+ mwana wa Gera akutuluka ndipo anali kulankhula mawu onyoza.+
13 Pamenepo Davide ndi amuna amene anali kuyenda naye anapitiriza kuyenda mumsewu. Simeyi anali kuyenda m’mbali mwa phiri pafupi ndi Davide ndipo anali kuyenda akulankhula mawu onyoza.+ Iye analinso kuponya miyala akuyenda m’mbali mwa phirimo pafupi ndi Davide ndiponso anali kuwaza fumbi lambiri.+