Levitiko 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “‘Usavule mkazi wa bambo ako,+ chifukwa kumeneko n’kuvula bambo ako. Levitiko 20:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mwamuna wogona ndi mkazi wa bambo ake, wavula* bambo ake.+ Mwamuna ndi mkaziyo aziphedwa ndithu. Mlandu wa magazi awo ukhale wa iwo eni. 2 Samueli 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Yehova wanena kuti, ‘Taona, ndikukugwetsera tsoka m’nyumba yako yomwe.+ Ndidzatenga akazi ako iwe ukuona ndi kuwapereka kwa mwamuna wina,+ ndipo iye adzagona ndi akazi ako anthu onse akuona.+ 1 Mafumu 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mfumu Solomo itamva zimenezi inafunsa mayi ake kuti: “N’chifukwa chiyani mukum’pemphera Adoniyayu Abisagi Msunemu? M’pemphereninso ufumu+ (chifukwa iye ndi mkulu wanga).+ Mupemphereni ufumu Adoniyayo. Mupempherenso wansembe Abiyatara+ ndi Yowabu+ mwana wa Zeruya.”+ Yobu 31:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mkazi wanga aperere ufa mwamuna wina,Ndipo amuna ena agone naye.+
11 Mwamuna wogona ndi mkazi wa bambo ake, wavula* bambo ake.+ Mwamuna ndi mkaziyo aziphedwa ndithu. Mlandu wa magazi awo ukhale wa iwo eni.
11 Ndiyeno Yehova wanena kuti, ‘Taona, ndikukugwetsera tsoka m’nyumba yako yomwe.+ Ndidzatenga akazi ako iwe ukuona ndi kuwapereka kwa mwamuna wina,+ ndipo iye adzagona ndi akazi ako anthu onse akuona.+
22 Mfumu Solomo itamva zimenezi inafunsa mayi ake kuti: “N’chifukwa chiyani mukum’pemphera Adoniyayu Abisagi Msunemu? M’pemphereninso ufumu+ (chifukwa iye ndi mkulu wanga).+ Mupemphereni ufumu Adoniyayo. Mupempherenso wansembe Abiyatara+ ndi Yowabu+ mwana wa Zeruya.”+