Genesis 35:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Isiraeli atamanga msasa+ m’dziko limenelo, Rubeni anagona ndi Biliha mkazi wamng’ono* wa bambo ake, ndipo Isiraeli anamva zimene zinachitikazo.+ Yakobo anali ndi ana aamuna 12. Levitiko 20:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mwamuna wogona ndi mkazi wa bambo ake, wavula* bambo ake.+ Mwamuna ndi mkaziyo aziphedwa ndithu. Mlandu wa magazi awo ukhale wa iwo eni. Deuteronomo 22:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “Pasapezeke mwamuna aliyense wotenga mkazi wa bambo ake kuopera kuti angavule bambo akewo.+ Deuteronomo 27:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “‘Wotembereredwa ndi munthu wogona ndi mkazi wa bambo ake, chifukwa wavula bambo akewo.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’) 2 Samueli 16:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pamenepo Ahitofeli anauza Abisalomu kuti: “Ugone ndi adzakazi a bambo ako+ amene wawasiya kuti azisamalira nyumba.+ Ukatero Aisiraeli onse adzamva kuti wadzinunkhitsa+ pamaso pa bambo ako,+ ndipo manja+ a anthu onse amene ali ndi iwe adzalimba ndithu.” 1 Akorinto 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mbiri yamvekatu kuti pakuchitika dama*+ pakati panu, ndipo dama lake ndi loti ngakhale anthu a mitundu ina sachita. Akuti mwamuna wina watengana ndi mkazi wa bambo ake.+
22 Isiraeli atamanga msasa+ m’dziko limenelo, Rubeni anagona ndi Biliha mkazi wamng’ono* wa bambo ake, ndipo Isiraeli anamva zimene zinachitikazo.+ Yakobo anali ndi ana aamuna 12.
11 Mwamuna wogona ndi mkazi wa bambo ake, wavula* bambo ake.+ Mwamuna ndi mkaziyo aziphedwa ndithu. Mlandu wa magazi awo ukhale wa iwo eni.
20 “‘Wotembereredwa ndi munthu wogona ndi mkazi wa bambo ake, chifukwa wavula bambo akewo.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’)
21 Pamenepo Ahitofeli anauza Abisalomu kuti: “Ugone ndi adzakazi a bambo ako+ amene wawasiya kuti azisamalira nyumba.+ Ukatero Aisiraeli onse adzamva kuti wadzinunkhitsa+ pamaso pa bambo ako,+ ndipo manja+ a anthu onse amene ali ndi iwe adzalimba ndithu.”
5 Mbiri yamvekatu kuti pakuchitika dama*+ pakati panu, ndipo dama lake ndi loti ngakhale anthu a mitundu ina sachita. Akuti mwamuna wina watengana ndi mkazi wa bambo ake.+