Genesis 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako Mulungu anati: “M’madzi mukhale zamoyo zambirimbiri,+ ndiponso zolengedwa zouluka ziuluke m’mlengalenga mwa dziko lapansi.”+ Yobu 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma funsa nyama zoweta ndipo zikulangiza.+Komanso zouluka zam’mlengalenga, ndipo zikuuza.+ Miyambo 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iye akulondola mkaziyo mpaka muvi utaboola chiwindi* chake,+ ngati mbalame yothamangira kumsampha,+ ndipo iye sakudziwa kuti zikukhudza moyo wake.+ Miyambo 30:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Njira ya chiwombankhanga m’mlengalenga, njira ya njoka pamwala, njira ya ngalawa pakatikati pa nyanja,+ ndiponso njira ya mwamuna ndi mtsikana.+
20 Kenako Mulungu anati: “M’madzi mukhale zamoyo zambirimbiri,+ ndiponso zolengedwa zouluka ziuluke m’mlengalenga mwa dziko lapansi.”+
23 Iye akulondola mkaziyo mpaka muvi utaboola chiwindi* chake,+ ngati mbalame yothamangira kumsampha,+ ndipo iye sakudziwa kuti zikukhudza moyo wake.+
19 Njira ya chiwombankhanga m’mlengalenga, njira ya njoka pamwala, njira ya ngalawa pakatikati pa nyanja,+ ndiponso njira ya mwamuna ndi mtsikana.+