1 Mafumu 12:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiyeno chifaniziro cha ng’ombe chimodzi anakachiika ku Beteli,+ china anakachiika ku Dani.+ 2 Mafumu 10:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kungoti iye sanasiye kutsatira machimo a Yerobowamu+ mwana wa Nebati amene anachimwitsa nawo Isiraeli.+ Machimo ake anali kulambira ana a ng’ombe agolide.+ Mmodzi wa ana a ng’ombe agolidewo anali ku Beteli, ndipo wina ku Dani.+
29 Kungoti iye sanasiye kutsatira machimo a Yerobowamu+ mwana wa Nebati amene anachimwitsa nawo Isiraeli.+ Machimo ake anali kulambira ana a ng’ombe agolide.+ Mmodzi wa ana a ng’ombe agolidewo anali ku Beteli, ndipo wina ku Dani.+