Yeremiya 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yehova anandiuza kuti: “Ngakhale Mose+ ndi Samueli+ akanaima pamaso panga, anthu awa sindikanawakomera mtima.+ Ndikanawapitikitsa pamaso panga kuti achoke.+ Maliro 3:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 “Ife taphwanya malamulo. Tachita zinthu zopanduka+ ndipo inu simunatikhululukire.+ Ezekieli 33:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Choncho auze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Inu mumadya nyama limodzi ndi magazi ake,+ mumayang’anitsitsa mafano anu onyansa+ ndipo mumakhetsa magazi.+ Kodi pamenepa ndinu oyenera kutenga dzikoli kuti likhale lanu?+
15 Yehova anandiuza kuti: “Ngakhale Mose+ ndi Samueli+ akanaima pamaso panga, anthu awa sindikanawakomera mtima.+ Ndikanawapitikitsa pamaso panga kuti achoke.+
25 “Choncho auze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Inu mumadya nyama limodzi ndi magazi ake,+ mumayang’anitsitsa mafano anu onyansa+ ndipo mumakhetsa magazi.+ Kodi pamenepa ndinu oyenera kutenga dzikoli kuti likhale lanu?+