Deuteronomo 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mudzatenthe zifaniziro zogoba za milungu yawo.+ Usadzalakelake siliva ndi golide wawo+ kapena kudzitengera zinthu zimenezi,+ kuopera kuti zingakutchere msampha,+ chifukwa zimenezi ndi zonyansa+ kwa Yehova Mulungu wako. 2 Samueli 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pa nthawiyi, Afilisiti anasiya mafano awo+ kumeneko, choncho Davide ndi anthu ake anawatenga.+ 2 Mafumu 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Atentha milungu yawo pamoto, chifukwa sinali milungu,+ koma ntchito ya manja a anthu,+ mitengo ndi miyala, n’chifukwa chake anaiwononga.
25 Mudzatenthe zifaniziro zogoba za milungu yawo.+ Usadzalakelake siliva ndi golide wawo+ kapena kudzitengera zinthu zimenezi,+ kuopera kuti zingakutchere msampha,+ chifukwa zimenezi ndi zonyansa+ kwa Yehova Mulungu wako.
18 Atentha milungu yawo pamoto, chifukwa sinali milungu,+ koma ntchito ya manja a anthu,+ mitengo ndi miyala, n’chifukwa chake anaiwononga.