Salimo 115:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mafano awo ndi opangidwa ndi siliva ndi golide,+Ntchito ya manja a munthu wochokera kufumbi.+ Yeremiya 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Miyambo ya anthu amenewa+ ndi yopanda pake, chifukwa mmisiri amagwetsa mtengo+ m’nkhalango ndi kusema fano pogwiritsa ntchito sompho.+ Machitidwe 17:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Popeza kuti ndife mbadwa za Mulungu,+ tisaganize kuti Mulunguyo+ ali ngati golide, siliva, mwala kapena chilichonse chosemedwa mwa luso ndi nzeru za munthu.+
3 Miyambo ya anthu amenewa+ ndi yopanda pake, chifukwa mmisiri amagwetsa mtengo+ m’nkhalango ndi kusema fano pogwiritsa ntchito sompho.+
29 “Popeza kuti ndife mbadwa za Mulungu,+ tisaganize kuti Mulunguyo+ ali ngati golide, siliva, mwala kapena chilichonse chosemedwa mwa luso ndi nzeru za munthu.+