-
Yesaya 44:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Ndine amene ndimachititsa mawu a mtumiki wanga kukwaniritsidwa ndiponso amene ndimakwaniritsa mawu onse amene atumiki anga analengeza.+ Ndine amene ndikunena za Yerusalemu kuti, ‘Muzidzakhala anthu.’+ Ndikunenanso za mizinda ya ku Yuda kuti, ‘Idzamangidwanso,+ ndipo malo ake osakazidwa ndidzawamanganso.’+
-