Numeri 23:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mulungu si munthu, woti anganene mabodza,+Si mwana wa munthu, woti angadzimve kuti ali ndi mlandu.+Kodi ananenapo kanthu koma osachita,Analankhulapo kanthu kodi koma osakwaniritsa?+ Yesaya 46:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ine ndi amene ndidzaitane mbalame yodya nyama kuchokera kotulukira dzuwa.+ Ndidzaitana munthu kuti adzachite zolingalira zanga kuchokera kutali.+ Ineyo ndalankhula ndipo ndidzazichita.+ Ndakonza zimenezi ndipo ndidzazichitadi.+ Aheberi 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamene Mulungu analonjeza Abulahamu,+ analumbira pa dzina lake+ chifukwa panalibe wina wamkulu kwa iye amene akanamulumbirira.
19 Mulungu si munthu, woti anganene mabodza,+Si mwana wa munthu, woti angadzimve kuti ali ndi mlandu.+Kodi ananenapo kanthu koma osachita,Analankhulapo kanthu kodi koma osakwaniritsa?+
11 Ine ndi amene ndidzaitane mbalame yodya nyama kuchokera kotulukira dzuwa.+ Ndidzaitana munthu kuti adzachite zolingalira zanga kuchokera kutali.+ Ineyo ndalankhula ndipo ndidzazichita.+ Ndakonza zimenezi ndipo ndidzazichitadi.+
13 Pamene Mulungu analonjeza Abulahamu,+ analumbira pa dzina lake+ chifukwa panalibe wina wamkulu kwa iye amene akanamulumbirira.