-
1 Samueli 10:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ukachoka pamenepo ufika kuphiri la Mulungu woona,+ kumene kuli mudzi wa asilikali+ a Afilisiti. Ndiyeno zimene zichitike n’zakuti, poyandikira mzindawo, ukumana ndi kagulu ka aneneri+ akuchokera kumalo okwezeka,+ akulankhula monga aneneri. Patsogolo pawo pakhala pali choimbira cha zingwe,+ maseche,+ chitoliro+ ndi zeze.+
-