1 Mbiri 15:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chotero Alevi anatenga Hemani+ mwana wa Yoweli n’kumuika pamalo ake. Kenako, pa abale ake, anatengapo Asafu+ mwana wa Berekiya n’kumuika pamalo ake. Pa abale awo, ana a Merari, anatengapo Etani+ mwana wa Kusaya n’kumuika pamalo ake.
17 Chotero Alevi anatenga Hemani+ mwana wa Yoweli n’kumuika pamalo ake. Kenako, pa abale ake, anatengapo Asafu+ mwana wa Berekiya n’kumuika pamalo ake. Pa abale awo, ana a Merari, anatengapo Etani+ mwana wa Kusaya n’kumuika pamalo ake.