25 Ndipo Davide ndi atsogoleri+ a magulu a anthu otumikira,+ anapatula ena mwa ana a Asafu, a Hemani,+ ndi a Yedutuni,+ kuti azitumikira. Amuna atatuwa anali kulosera ndi azeze,+ zoimbira za zingwe,+ ndi zinganga.+ Mwa ana awo anatengamo amuna ena n’kuwaika pa udindo kuti azitumikira.