1 Mafumu 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma iweyo unayamba kuchita zinthu zoipa kwambiri kuposa onse amene anakhalapo iwe usanakhale. Unadzipangiranso mulungu wina+ ndi zifaniziro zopangidwa ndi zitsulo zosungunula+ kuti undikwiyitse,+ ndipo wandikankhira ineyo kumbuyo kwako.+ Hoseya 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tamverani mawu a Yehova inu ana a Isiraeli. Yehova ali ndi mlandu ndi anthu okhala m’dzikoli,+ chifukwa m’dzikoli mulibe choonadi,+ kukoma mtima kosatha, ndiponso anthu a m’dzikoli amachita zinthu ngati kuti sadziwa Mulungu.+
9 Koma iweyo unayamba kuchita zinthu zoipa kwambiri kuposa onse amene anakhalapo iwe usanakhale. Unadzipangiranso mulungu wina+ ndi zifaniziro zopangidwa ndi zitsulo zosungunula+ kuti undikwiyitse,+ ndipo wandikankhira ineyo kumbuyo kwako.+
4 Tamverani mawu a Yehova inu ana a Isiraeli. Yehova ali ndi mlandu ndi anthu okhala m’dzikoli,+ chifukwa m’dzikoli mulibe choonadi,+ kukoma mtima kosatha, ndiponso anthu a m’dzikoli amachita zinthu ngati kuti sadziwa Mulungu.+