1 Mafumu 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Panali zombo zimene Mfumu Solomo inapanga ku Ezioni-geberi,+ pafupi ndi Eloti,+ pagombe la Nyanja Yofiira m’dziko la Edomu.+ 2 Mafumu 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pa nthawiyo, Rezini mfumu ya Siriya anabwezeretsa mzinda wa Elati+ ku Edomu. Kenako anachotsa Ayuda mu Elati ndipo Aedomu analowa n’kumakhalamo. Iwo akukhalabe komweko mpaka lero. 2 Mbiri 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Panali pa nthawi imeneyi pamene Solomo anapita ku Ezioni-geberi+ ndi ku Eloti,+ kugombe la nyanja m’dziko la Edomu.+
26 Panali zombo zimene Mfumu Solomo inapanga ku Ezioni-geberi,+ pafupi ndi Eloti,+ pagombe la Nyanja Yofiira m’dziko la Edomu.+
6 Pa nthawiyo, Rezini mfumu ya Siriya anabwezeretsa mzinda wa Elati+ ku Edomu. Kenako anachotsa Ayuda mu Elati ndipo Aedomu analowa n’kumakhalamo. Iwo akukhalabe komweko mpaka lero.
17 Panali pa nthawi imeneyi pamene Solomo anapita ku Ezioni-geberi+ ndi ku Eloti,+ kugombe la nyanja m’dziko la Edomu.+