19 Musamale kuti musakweze maso anu kuthambo ndi kuona dzuwa, mwezi ndi nyenyezi, khamu lonse la zinthu zakuthambo, zimene Yehova Mulungu wanu wazipereka kwa anthu onse okhala pansi pa thambo lonse,+ n’kunyengeka nazo, kuzigwadira ndi kuyamba kuzitumikira.+