Ekisodo 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kodi ukudzikwezabe pa anthu anga, pokana kuwalola kuti achoke?+ 2 Mafumu 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma iwo sanamvere. M’malomwake anaumitsa makosi awo,+ ngati mmene makolo awo anaumitsira makosi awo. Makolo awowo sanasonyeze chikhulupiriro+ mwa Yehova Mulungu wawo. Nehemiya 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Koma iwo, makolo athu, anachita zinthu modzikuza+ moti anaumitsa khosi lawo+ ndipo sanamvere malamulo anu. Miyambo 28:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Wodala ndi munthu amene amaopa Mulungu nthawi zonse,+ koma woumitsa mtima wake adzagwera m’tsoka.+ Miyambo 29:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Munthu wodzudzulidwa kawirikawiri+ koma amene amaumitsa khosi lake,+ adzathyoledwa mwadzidzidzi ndipo akadzatero sadzachira.+
14 Koma iwo sanamvere. M’malomwake anaumitsa makosi awo,+ ngati mmene makolo awo anaumitsira makosi awo. Makolo awowo sanasonyeze chikhulupiriro+ mwa Yehova Mulungu wawo.
16 “Koma iwo, makolo athu, anachita zinthu modzikuza+ moti anaumitsa khosi lawo+ ndipo sanamvere malamulo anu.
14 Wodala ndi munthu amene amaopa Mulungu nthawi zonse,+ koma woumitsa mtima wake adzagwera m’tsoka.+
29 Munthu wodzudzulidwa kawirikawiri+ koma amene amaumitsa khosi lake,+ adzathyoledwa mwadzidzidzi ndipo akadzatero sadzachira.+