Ekisodo 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo Mose ndi Aroni anachita zozizwitsa zonsezi pamaso pa Farao.+ Koma Yehova analola Farao kuumitsa mtima wake, moti sanalole ana a Isiraeli kuchoka m’dziko lake.+ 2 Mbiri 36:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kuwonjezera pamenepo, Zedekiya anapandukira Mfumu Nebukadinezara+ yomwe inali itamulumbiritsa kwa Mulungu,+ ndipo anapitiriza kuumitsa khosi lake ndi mtima wake+ kuti asabwerere kwa Yehova Mulungu wa Isiraeli. Salimo 75:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Musakweze nyanga yanu pamwamba.Musalankhule modzikuza.+ Yeremiya 17:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma iwo sanamvere kapena kutchera khutu+ moti anapitiriza kuumitsa khosi+ lawo kuti asamve ndi kulandira mwambo.”’*+
10 Ndipo Mose ndi Aroni anachita zozizwitsa zonsezi pamaso pa Farao.+ Koma Yehova analola Farao kuumitsa mtima wake, moti sanalole ana a Isiraeli kuchoka m’dziko lake.+
13 Kuwonjezera pamenepo, Zedekiya anapandukira Mfumu Nebukadinezara+ yomwe inali itamulumbiritsa kwa Mulungu,+ ndipo anapitiriza kuumitsa khosi lake ndi mtima wake+ kuti asabwerere kwa Yehova Mulungu wa Isiraeli.
23 Koma iwo sanamvere kapena kutchera khutu+ moti anapitiriza kuumitsa khosi+ lawo kuti asamve ndi kulandira mwambo.”’*+