Levitiko 26:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Mizinda yanu ndidzaiwononga ndi lupanga+ ndipo malo anu opatulika adzakhala opanda anthu,+ komanso sindidzalandira nsembe zanu zafungo lokhazika mtima pansi.+ Deuteronomo 28:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Yehova adzakuchititsani kuti mugonje pamaso pa adani anu.+ Pokamenyana nawo nkhondo mudzadutsa njira imodzi, koma pothawa pamaso pawo mudzadutsa njira 7. Mudzakhala chinthu chonyansa kwa mafumu onse a dziko lapansi.+ Salimo 79:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Apereka mitembo ya atumiki anu kwa mbalame kuti chikhale chakudya chawo.+Matupi a okhulupirika anu awapereka kwa zilombo zakutchire.+
31 Mizinda yanu ndidzaiwononga ndi lupanga+ ndipo malo anu opatulika adzakhala opanda anthu,+ komanso sindidzalandira nsembe zanu zafungo lokhazika mtima pansi.+
25 Yehova adzakuchititsani kuti mugonje pamaso pa adani anu.+ Pokamenyana nawo nkhondo mudzadutsa njira imodzi, koma pothawa pamaso pawo mudzadutsa njira 7. Mudzakhala chinthu chonyansa kwa mafumu onse a dziko lapansi.+
2 Apereka mitembo ya atumiki anu kwa mbalame kuti chikhale chakudya chawo.+Matupi a okhulupirika anu awapereka kwa zilombo zakutchire.+