-
Deuteronomo 12:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Ndiyeno malo amene Yehova Mulungu wako adzasankha kuikapo dzina lake+ akadzakhala kutali kwambiri ndi iwe, uzidzapha zina mwa ng’ombe zako kapena zina mwa nkhosa zako zimene Yehova wakupatsa, monga mmene ndakulamulira, ndipo uzidzadyera mumzinda mwako nyamazo, nthawi iliyonse imene mtima wako wafuna.+
-