Ezara 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako Tatenai bwanamkubwa wa kutsidya lina la Mtsinje,+ Setara-bozenai+ ndi anzawo anachita mogwirizana ndi mawu amene mfumu Dariyo inatumiza. Anachita zimenezi mwamsanga.
13 Kenako Tatenai bwanamkubwa wa kutsidya lina la Mtsinje,+ Setara-bozenai+ ndi anzawo anachita mogwirizana ndi mawu amene mfumu Dariyo inatumiza. Anachita zimenezi mwamsanga.