Ezara 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Izi n’zimene zinali m’kalata+ imene Tatenai+ bwanamkubwa wa kutsidya lina la Mtsinje,+ Setara-bozenai+ ndi anzake,+ ndiponso abwanamkubwa aang’ono amene anali kutsidya lina la Mtsinje, anatumiza kwa mfumu Dariyo.
6 Izi n’zimene zinali m’kalata+ imene Tatenai+ bwanamkubwa wa kutsidya lina la Mtsinje,+ Setara-bozenai+ ndi anzake,+ ndiponso abwanamkubwa aang’ono amene anali kutsidya lina la Mtsinje, anatumiza kwa mfumu Dariyo.