-
Numeri 15:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Ndiponso muzikapereka vinyo monga nsembe yachakumwa. Azikakhala wokwana gawo limodzi mwa magawo atatu a muyezo wa hini, monga fungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova.
-