1 Mbiri 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Oyamba kubwerera n’kukakhala ku cholowa chawo m’mizinda yawo anali Aisiraeli,+ ansembe,+ Alevi,+ ndi Anetini.+ Nehemiya 7:73 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 73 Ndiyeno ansembe,+ Alevi, alonda a pazipata, oimba,+ anthu ena onse pamodzi ndi Anetini+ ndi Isiraeli yense anapita kukakhala m’mizinda yawo.+ Pofika mwezi wa 7+ ana a Isiraeli anali atakhala m’mizinda yawo.+
2 Oyamba kubwerera n’kukakhala ku cholowa chawo m’mizinda yawo anali Aisiraeli,+ ansembe,+ Alevi,+ ndi Anetini.+
73 Ndiyeno ansembe,+ Alevi, alonda a pazipata, oimba,+ anthu ena onse pamodzi ndi Anetini+ ndi Isiraeli yense anapita kukakhala m’mizinda yawo.+ Pofika mwezi wa 7+ ana a Isiraeli anali atakhala m’mizinda yawo.+