Ezara 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ikhale ndi mizere itatu ya miyala yochita kuigubuduzira+ pamalopo ndi mzere umodzi wa matabwa.+ Ndalama zake zichokere kunyumba ya mfumu.+ Salimo 68:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chifukwa cha kachisi wanu yemwe ali ku Yerusalemu,+Mafumu adzabweretsa mphatso kwa inu.+
4 Ikhale ndi mizere itatu ya miyala yochita kuigubuduzira+ pamalopo ndi mzere umodzi wa matabwa.+ Ndalama zake zichokere kunyumba ya mfumu.+