-
Yobu 26:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Iye anakulunga madzi m’mitambo yake,+
Moti mitamboyo sing’ambika pansi pa madziwo.
-
8 Iye anakulunga madzi m’mitambo yake,+
Moti mitamboyo sing’ambika pansi pa madziwo.