Yobu 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma amuna inu ndinu onamizira anzanu.+Nonsenu ndinu madokotala opanda phindu.+ Yobu 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Kodi amuna inu musautsa moyo wanga mpaka liti,+Ndi kundilasa ndi mawu?+ Afilipi 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma oyambawo akutero chifukwa cha mtima wokonda mikangano,+ osati ndi cholinga chabwino. Pakuti akungofuna kundiwonjezera masautso+ m’ndende muno.
17 Koma oyambawo akutero chifukwa cha mtima wokonda mikangano,+ osati ndi cholinga chabwino. Pakuti akungofuna kundiwonjezera masautso+ m’ndende muno.