Yobu 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mofanana ndi zimenezi, amuna inu mwakhala opanda pake,+Mwaona zoopsa n’kuyamba kuchita mantha.+ Yobu 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ndamva zinthu zambiri ngati zimenezi.Nonsenu ndinu otonthoza onditopetsa!+ Yeremiya 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo akuyesa kuchiritsa mwachinyengo+ kuwonongeka kwa anthu anga ponena kuti, ‘Kuli mtendere! Kuli mtendere!’ pamene kulibe mtendere.+ Ezekieli 34:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Nkhosa zodwala simunazilimbitse+ ndipo zamatenda simunazichiritse. Yothyoka mwendo simunaimange mwendo wothyokawo. Nkhosa zomwazika simunazibweze ndipo zosochera simunazifufuze kuti muzipeze.+ Munali kuzilamulira mouma mtima komanso mwankhanza.+
14 Iwo akuyesa kuchiritsa mwachinyengo+ kuwonongeka kwa anthu anga ponena kuti, ‘Kuli mtendere! Kuli mtendere!’ pamene kulibe mtendere.+
4 Nkhosa zodwala simunazilimbitse+ ndipo zamatenda simunazichiritse. Yothyoka mwendo simunaimange mwendo wothyokawo. Nkhosa zomwazika simunazibweze ndipo zosochera simunazifufuze kuti muzipeze.+ Munali kuzilamulira mouma mtima komanso mwankhanza.+