Yobu 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mahema a anthu olanda amakhala opanda nkhawa,+Ndipo anthu okwiyitsa Mulungu amakhala pa mtendereWofanana ndi wa munthu amene watenga mulungu* m’manja mwake.+ Salimo 37:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Khala chete pamaso pa Yehova,+Ndipo umuyembekezere ndi mtima wako wonse.+Usapse mtima ndi aliyense amene zinthu zikumuyendera bwino,+Munthu amene akukwaniritsa zolinga zake zoipa.+ Salimo 73:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti ndinachitira nsanje anthu odzitukumula,+Ndikamaona mtendere wa anthu oipa.+ Salimo 73:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Onani! Awa ndi anthu oipa, amene akukhala mosatekeseka mpaka kalekale.+Iwo achulukitsa chuma chawo.+ Yeremiya 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu Yehova, ndinu Mulungu wolungama.+ Ndikabweretsa dandaulo kwa inu, ndipo ndikalankhula za chiweruzo chanu, mumachita chilungamo. Koma n’chifukwa chiyani anthu oipa, zinthu zikuwayendera bwino?+ N’chifukwa chiyani onse ochita chinyengo amakhala opanda nkhawa iliyonse?
6 Mahema a anthu olanda amakhala opanda nkhawa,+Ndipo anthu okwiyitsa Mulungu amakhala pa mtendereWofanana ndi wa munthu amene watenga mulungu* m’manja mwake.+
7 Khala chete pamaso pa Yehova,+Ndipo umuyembekezere ndi mtima wako wonse.+Usapse mtima ndi aliyense amene zinthu zikumuyendera bwino,+Munthu amene akukwaniritsa zolinga zake zoipa.+
12 Onani! Awa ndi anthu oipa, amene akukhala mosatekeseka mpaka kalekale.+Iwo achulukitsa chuma chawo.+
12 Inu Yehova, ndinu Mulungu wolungama.+ Ndikabweretsa dandaulo kwa inu, ndipo ndikalankhula za chiweruzo chanu, mumachita chilungamo. Koma n’chifukwa chiyani anthu oipa, zinthu zikuwayendera bwino?+ N’chifukwa chiyani onse ochita chinyengo amakhala opanda nkhawa iliyonse?