Yoswa 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Palibe amene adzatha kulimbana nawe masiku onse a moyo wako.+ Ndidzakhala nawe+ monga mmene ndinakhalira ndi Mose, sindidzakutaya kapena kukusiya ngakhale pang’ono.+ Salimo 94:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova sadzataya anthu ake,+Kapena kusiya cholowa chake.+ Mateyu 6:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “Chotero pitirizani kufunafuna ufumu choyamba ndi chilungamo chake,+ ndipo zina zonsezi zidzawonjezedwa kwa inu.+ Aheberi 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Moyo wanu ukhale wosakonda ndalama,+ koma mukhale okhutira+ ndi zimene muli nazo pa nthawiyo.+ Pakuti Mulungu anati: “Sindidzakusiyani kapena kukutayani ngakhale pang’ono.”+
5 Palibe amene adzatha kulimbana nawe masiku onse a moyo wako.+ Ndidzakhala nawe+ monga mmene ndinakhalira ndi Mose, sindidzakutaya kapena kukusiya ngakhale pang’ono.+
33 “Chotero pitirizani kufunafuna ufumu choyamba ndi chilungamo chake,+ ndipo zina zonsezi zidzawonjezedwa kwa inu.+
5 Moyo wanu ukhale wosakonda ndalama,+ koma mukhale okhutira+ ndi zimene muli nazo pa nthawiyo.+ Pakuti Mulungu anati: “Sindidzakusiyani kapena kukutayani ngakhale pang’ono.”+