Salimo 91:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mulungu wanena kuti: “Popeza wasonyeza kuti amandikonda,+Inenso ndidzamupulumutsa.+Ndidzamuteteza chifukwa wadziwa dzina langa.+ Yakobo 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Wodala ndi munthu wopirira mayesero,+ chifukwa akadzavomerezedwa, adzalandira mphoto* ya moyo,+ umene Yehova analonjeza onse omukonda.+
14 Mulungu wanena kuti: “Popeza wasonyeza kuti amandikonda,+Inenso ndidzamupulumutsa.+Ndidzamuteteza chifukwa wadziwa dzina langa.+
12 Wodala ndi munthu wopirira mayesero,+ chifukwa akadzavomerezedwa, adzalandira mphoto* ya moyo,+ umene Yehova analonjeza onse omukonda.+